Salimo 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Makolo athu ankadalira inu.+Iwo ankakudalirani ndipo inu munkawapulumutsa.+