Genesis 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu mʼmasomphenya kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+ Genesis 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abulamu anakhulupirira zimene Yehova anamuuza,+ ndipo Mulunguyo anamuona kuti ndi wolungama.+
15 Zimenezi zitachitika, Yehova analankhula ndi Abulamu mʼmasomphenya kuti: “Usaope+ Abulamu. Ine ndine chishango chako.+ Mphoto yako idzakhala yaikulu kwambiri.”+