Aheberi 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa cha chikhulupiriro, Abulahamu+ ataitanidwa, anamvera nʼkupita kumalo amene ankayembekezera kuwalandira ngati cholowa. Iye anapitadi, ngakhale kuti sankadziwa kumene akupita.+
8 Chifukwa cha chikhulupiriro, Abulahamu+ ataitanidwa, anamvera nʼkupita kumalo amene ankayembekezera kuwalandira ngati cholowa. Iye anapitadi, ngakhale kuti sankadziwa kumene akupita.+