Aheberi 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mwa chikhulupiriro, Abulahamu+ ataitanidwa, anamvera ndi kupita kumalo amene anali kuyembekezera kuwalandira monga cholowa. Iye anapitadi, ngakhale sanadziwe kumene anali kupita.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2020, ptsa. 3-4
8 Mwa chikhulupiriro, Abulahamu+ ataitanidwa, anamvera ndi kupita kumalo amene anali kuyembekezera kuwalandira monga cholowa. Iye anapitadi, ngakhale sanadziwe kumene anali kupita.+