Genesis 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo, Abulamu ananyamuka malinga ndi mmene Yehova anamuuzira, ndipo Loti ananyamuka naye limodzi. Pochoka ku Harana,+ Abulamu anali ndi zaka 75. Machitidwe 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+
4 Pamenepo, Abulamu ananyamuka malinga ndi mmene Yehova anamuuzira, ndipo Loti ananyamuka naye limodzi. Pochoka ku Harana,+ Abulamu anali ndi zaka 75.
2 Sitefano anati: “Amuna inu, abale anga ndi abambo anga, mvetserani! Mulungu waulemerero+ anaonekera kwa kholo lathu Abulahamu pamene anali ku Mesopotamiya, asanakakhale ku Harana.+