Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 106:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Koma Mulungu anawapulumutsa chifukwa cha dzina lake,+

      Kuti mphamvu zake zidziwike.+

  • Salimo 106:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iwo anaiwala Mulungu, Mpulumutsi wawo,+

      Amene anachita zinthu zazikulu ku Iguputo,+

  • Yesaya 45:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndithu, inu ndinu Mulungu yemwe amadzibisa,+ Mulungu wa Isiraeli, Mpulumutsi.+

  • Tito 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma mu nthawi yake, anapangitsa mawu ake kuonekera kudzera mu ulaliki umene ndinapatsidwa+ mwa lamulo la Mpulumutsi wathu,+ Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena