Yesaya 43:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndine Yehova.+ Popanda ine palibenso mpulumutsi wina.”+ Yesaya 60:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwe udzayamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+ ndipo udzayamwa bere la mafumu.+ Udzadziwadi kuti ine Yehova+ ndine Mpulumutsi wako,+ ndipo Wamphamvu+ wa Yakobo ndiye Wokuwombola.+ Tito 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma mu nthawi yake, anapangitsa mawu ake kuonekera kudzera mu ulaliki umene ndinapatsidwa+ mwa lamulo la Mpulumutsi wathu,+ Mulungu.
16 Iwe udzayamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+ ndipo udzayamwa bere la mafumu.+ Udzadziwadi kuti ine Yehova+ ndine Mpulumutsi wako,+ ndipo Wamphamvu+ wa Yakobo ndiye Wokuwombola.+
3 Koma mu nthawi yake, anapangitsa mawu ake kuonekera kudzera mu ulaliki umene ndinapatsidwa+ mwa lamulo la Mpulumutsi wathu,+ Mulungu.