Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+ Hoseya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Panalibe Mulungu wina amene unali kumudziwa kupatulapo ine. Panalibenso mpulumutsi wina kupatulapo ine.+ 1 Timoteyo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zimenezi ndi zabwino ndiponso ndi zovomerezeka+ kwa Mpulumutsi wathu Mulungu,+ Yuda 25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 kwa iyeyo, Mulungu yekhayo amenenso ndi Mpulumutsi wathu+ mwa Yesu Khristu+ Ambuye wathu, kukhale ulemerero,+ ukulu, mphamvu+ ndi ulamuliro,+ kuchokera kalekale+ kufikira panopa, mpaka ku nthawi yonse yomka muyaya.+ Ame.+
2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
4 “Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Panalibe Mulungu wina amene unali kumudziwa kupatulapo ine. Panalibenso mpulumutsi wina kupatulapo ine.+
25 kwa iyeyo, Mulungu yekhayo amenenso ndi Mpulumutsi wathu+ mwa Yesu Khristu+ Ambuye wathu, kukhale ulemerero,+ ukulu, mphamvu+ ndi ulamuliro,+ kuchokera kalekale+ kufikira panopa, mpaka ku nthawi yonse yomka muyaya.+ Ame.+