Ekisodo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndine Yehova Mulungu wako,+ amene ndinakutulutsa m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.+ Levitiko 11:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ine ndine Yehova amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti ndikusonyezeni kuti ndine Mulungu.+ Muzikhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Salimo 81:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,+Amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.+Tsegulani pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+ Hoseya 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Koma ndidzakuchititsa kukhala m’mahema ngati pa masiku achikondwerero.
45 Ine ndine Yehova amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti ndikusonyezeni kuti ndine Mulungu.+ Muzikhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+
10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,+Amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.+Tsegulani pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+
9 “Ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Koma ndidzakuchititsa kukhala m’mahema ngati pa masiku achikondwerero.