Ekisodo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndine Yehova Mulungu wako,+ amene ndinakutulutsa m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.+ Hoseya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Panalibe Mulungu wina amene unali kumudziwa kupatulapo ine. Panalibenso mpulumutsi wina kupatulapo ine.+
4 “Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+ Panalibe Mulungu wina amene unali kumudziwa kupatulapo ine. Panalibenso mpulumutsi wina kupatulapo ine.+