Salimo 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Makolo athu anali kudalira inu.+Iwo anali kudalira inu ndipo munali kuwapulumutsa.+ Yeremiya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu chiyembekezo cha Isiraeli,+ Mpulumutsi wake+ pa nthawi ya nsautso,+ n’chifukwa chiyani mukukhala ngati mlendo m’dzikoli? N’chifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wapaulendo amene wapatuka kuti agone usiku umodzi wokha?+ Yeremiya 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Yehova, chiyembekezo cha Isiraeli,+ onse amene akukusiyani adzachita manyazi.+ Mayina a anthu onse okupandukirani+ adzalembedwa pafumbi chifukwa asiya Yehova magwero a madzi amoyo.+
8 Inu chiyembekezo cha Isiraeli,+ Mpulumutsi wake+ pa nthawi ya nsautso,+ n’chifukwa chiyani mukukhala ngati mlendo m’dzikoli? N’chifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wapaulendo amene wapatuka kuti agone usiku umodzi wokha?+
13 Inu Yehova, chiyembekezo cha Isiraeli,+ onse amene akukusiyani adzachita manyazi.+ Mayina a anthu onse okupandukirani+ adzalembedwa pafumbi chifukwa asiya Yehova magwero a madzi amoyo.+