Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 33:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mzimu wa Mulungu unandiumba,+

      Mpweya wa Wamphamvuyonse unandipatsa moyo.+

  • Yeremiya 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 ‘chifukwa pali zinthu ziwiri zoipa zimene anthu anga achita: Iwo asiya ine+ kasupe wa madzi amoyo,+ ndipo akumba zitsime zawozawo, zitsime zong’ambika zimene sizingasunge madzi.’

  • Machitidwe 17:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pakuti chifukwa cha iye tili ndi moyo, timayenda ndipo tilipo,+ monga mmene andakatulo+ ena pakati panu anenera kuti, ‘Pakuti ndife mbadwa zake.’

  • Chivumbulutso 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena