Salimo 49:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zokhumba za mtima wawo n’zakuti nyumba zawo zikhalebe mpaka kalekale,+Mahema awo akhalebe ku mibadwomibadwo.+Malo awo amawatcha mayina awo.+ Danieli 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+ Yohane 5:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mungakhulupirire bwanji, pamene mumalandira ulemerero+ kuchokera kwa anthu anzanu, koma osayesetsa kupeza ulemerero wochokera kwa Mulungu yekhayo?+
11 Zokhumba za mtima wawo n’zakuti nyumba zawo zikhalebe mpaka kalekale,+Mahema awo akhalebe ku mibadwomibadwo.+Malo awo amawatcha mayina awo.+
30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+
44 Mungakhulupirire bwanji, pamene mumalandira ulemerero+ kuchokera kwa anthu anzanu, koma osayesetsa kupeza ulemerero wochokera kwa Mulungu yekhayo?+