Salimo 73:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kudzikweza kwawo kwafika kumwamba,+Akuyendayenda padziko lapansi ndipo lilime lawo likunena zilizonse zimene akufuna.+
9 Kudzikweza kwawo kwafika kumwamba,+Akuyendayenda padziko lapansi ndipo lilime lawo likunena zilizonse zimene akufuna.+