Ekisodo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Farao anati: “Yehova ndani+ kuti ndimvere mawu ake, ndi kulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikum’dziwa Yehova ngakhale pang’ono,+ komanso, sindilola kuti Aisiraeli apite.”+ Chivumbulutso 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chilombocho chinatsegula pakamwa pake n’kumanyoza Mulungu,+ dzina lake ndi malo ake okhala, ndiponso amene akukhala kumwamba.+
2 Koma Farao anati: “Yehova ndani+ kuti ndimvere mawu ake, ndi kulola Aisiraeli kuti apite?+ Ine sindikum’dziwa Yehova ngakhale pang’ono,+ komanso, sindilola kuti Aisiraeli apite.”+
6 Chilombocho chinatsegula pakamwa pake n’kumanyoza Mulungu,+ dzina lake ndi malo ake okhala, ndiponso amene akukhala kumwamba.+