-
Salimo 49:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Zimene mtima wawo umalakalaka nʼzakuti nyumba zawo zikhale mpaka kalekale,
Matenti awo akhale ku mibadwomibadwo.
Ndipo malo awo amawapatsa mayina awo.
-