Salimo 49:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zokhumba za mtima wawo n’zakuti nyumba zawo zikhalebe mpaka kalekale,+Mahema awo akhalebe ku mibadwomibadwo.+Malo awo amawatcha mayina awo.+
11 Zokhumba za mtima wawo n’zakuti nyumba zawo zikhalebe mpaka kalekale,+Mahema awo akhalebe ku mibadwomibadwo.+Malo awo amawatcha mayina awo.+