Yesaya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+ anthu olemedwa ndi zolakwa, mbewu yochita zoipa,+ ana obweretsa chiwonongeko.+ Iwo amusiya Yehova.+ Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu,+ ndipo abwerera m’mbuyo.+ Yeremiya 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Iwe wandisiya,’+ watero Yehova. ‘Ukundifulatira ndi kundichokera.+ Choncho nditambasula dzanja langa kuti ndikukanthe ndi kukuwononga.+ Ndatopa nako kukumvera chisoni.+ Yakobo 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu aliyense amayesedwa mwa kukopedwa ndi kukodwa m’chilakolako chake.+
4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+ anthu olemedwa ndi zolakwa, mbewu yochita zoipa,+ ana obweretsa chiwonongeko.+ Iwo amusiya Yehova.+ Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu,+ ndipo abwerera m’mbuyo.+
6 “‘Iwe wandisiya,’+ watero Yehova. ‘Ukundifulatira ndi kundichokera.+ Choncho nditambasula dzanja langa kuti ndikukanthe ndi kukuwononga.+ Ndatopa nako kukumvera chisoni.+