Yeremiya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo ine ndidzapereka zigamulo zanga pa Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda chifukwa cha zoipa zawo zonse,+ pakuti iwo andisiya ine+ ndipo amafukiza nsembe zautsi kwa milungu ina+ ndi kugwadira ntchito za manja awo.’+ Yeremiya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ‘chifukwa pali zinthu ziwiri zoipa zimene anthu anga achita: Iwo asiya ine+ kasupe wa madzi amoyo,+ ndipo akumba zitsime zawozawo, zitsime zong’ambika zimene sizingasunge madzi.’
16 Ndipo ine ndidzapereka zigamulo zanga pa Yerusalemu ndi mizinda ya Yuda chifukwa cha zoipa zawo zonse,+ pakuti iwo andisiya ine+ ndipo amafukiza nsembe zautsi kwa milungu ina+ ndi kugwadira ntchito za manja awo.’+
13 ‘chifukwa pali zinthu ziwiri zoipa zimene anthu anga achita: Iwo asiya ine+ kasupe wa madzi amoyo,+ ndipo akumba zitsime zawozawo, zitsime zong’ambika zimene sizingasunge madzi.’