Yesaya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo. Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.+ Machitidwe 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho iwo anapanga mwana wa ng’ombe m’masiku amenewo,+ ndi kubweretsa nsembe kwa fano limenelo. Pamenepo anasangalala ndi ntchito za manja awo.+
8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo. Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.+
41 Choncho iwo anapanga mwana wa ng’ombe m’masiku amenewo,+ ndi kubweretsa nsembe kwa fano limenelo. Pamenepo anasangalala ndi ntchito za manja awo.+