Ekisodo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho pa tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mamawa, ndi kuyamba kupereka nsembe zopsereza ndi zachiyanjano. Atatero, iwo anakhala pansi ndi kudya ndiponso kumwa. Kenako anaimirira n’kuyamba kusangalala.+ Salimo 106:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo anapanganso mwana wa ng’ombe ku Horebe,+Ndipo anaweramira chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+
6 Choncho pa tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mamawa, ndi kuyamba kupereka nsembe zopsereza ndi zachiyanjano. Atatero, iwo anakhala pansi ndi kudya ndiponso kumwa. Kenako anaimirira n’kuyamba kusangalala.+
19 Iwo anapanganso mwana wa ng’ombe ku Horebe,+Ndipo anaweramira chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+