Machitidwe 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho iwo anapanga mwana wa ng’ombe m’masiku amenewo,+ ndi kubweretsa nsembe kwa fano limenelo. Pamenepo anasangalala ndi ntchito za manja awo.+ 1 Akorinto 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo tisapembedze mafano, mmene ena mwa iwo anachitira,+ monga mmene Malemba amanenera kuti: “Anthu anakhala pansi ndi kudya ndiponso kumwa. Kenako anaimirira n’kuyamba kusangalala.”+
41 Choncho iwo anapanga mwana wa ng’ombe m’masiku amenewo,+ ndi kubweretsa nsembe kwa fano limenelo. Pamenepo anasangalala ndi ntchito za manja awo.+
7 Ndipo tisapembedze mafano, mmene ena mwa iwo anachitira,+ monga mmene Malemba amanenera kuti: “Anthu anakhala pansi ndi kudya ndiponso kumwa. Kenako anaimirira n’kuyamba kusangalala.”+