Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kumeneko mudzatumikira milungu+ yopangidwa ndi manja a anthu, milungu ya mtengo ndi mwala,+ imene siingaone, kumva, kudya kapena kununkhiza.+

  • Salimo 115:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mafano awo ndi opangidwa ndi siliva ndi golide,+

      Ntchito ya manja a munthu wochokera kufumbi.+

  • Hoseya 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano anthu ake akuchita machimo ena ndipo akugwiritsa ntchito siliva wawo popanga zifanizo zachitsulo chosungunula.+ Zifanizo zimenezo ndi mafano opangidwa mogwirizana ndi maganizo awo,+ koma zonsezi ndi ntchito za amisiri.+ Iwo amauza mafanowo kuti, ‘Amuna opereka nsembe apsompsone mafano a ana ang’ombe.’+

  • Chivumbulutso 9:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma anthu ena onse amene sanaphedwe ndi miliri imeneyi, sanalape ntchito za manja awo.+ Sanalape kulambira ziwanda+ ndi mafano agolide, asiliva,+ amkuwa, amwala, ndi amtengo, mafano amene sangathe kuona, kumva, kapena kuyenda.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena