Salimo 115:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mafano awo ndi opangidwa ndi siliva ndi golide,+Ntchito ya manja a munthu wochokera kufumbi.+ Salimo 135:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mafano a anthu a mitundu ina ndi opangidwa ndi siliva ndi golide,+Ntchito ya manja a munthu wochokera kufumbi.+
15 Mafano a anthu a mitundu ina ndi opangidwa ndi siliva ndi golide,+Ntchito ya manja a munthu wochokera kufumbi.+