Yesaya 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali anthu amene amakhuthula golide m’zikwama, ndi kuyeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo iye amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kuweramira ndi kugwadira mulunguyo.+ Machitidwe 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+
6 Pali anthu amene amakhuthula golide m’zikwama, ndi kuyeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo iye amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kuweramira ndi kugwadira mulunguyo.+
29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+