5 Mukangomva kulira kwa lipenga, chitoliro, zeze wamng’ono, zoimbira zosiyanasiyana za zingwe, chitoliro chathumba ndi zipangizo zosiyanasiyana zoimbira,+ mugwade ndi kuwerama mpaka nkhope zanu pansi ndi kulambira fano lagolide limene mfumu Nebukadinezara yaimika.