Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kumeneko mudzatumikira milungu+ yopangidwa ndi manja a anthu, milungu ya mtengo ndi mwala,+ imene siingaone, kumva, kudya kapena kununkhiza.+

  • Yesaya 40:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mmisiri wapanga chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+ Mmisiri wina wa zitsulo wachikuta ndi golide,+ ndipo akuchipangira matcheni asiliva.+

  • Yesaya 44:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma mtengo wotsalawo wapangira mulungu, wapangira chifaniziro chake chosema. Wachiweramira ndi kuchigwadira n’kumapemphera pamaso pake kuti: “Ndipulumutseni, pakuti ndinu mulungu wanga.”+

  • Yeremiya 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Miyambo ya anthu amenewa+ ndi yopanda pake, chifukwa mmisiri amagwetsa mtengo+ m’nkhalango ndi kusema fano pogwiritsa ntchito sompho.+

  • Machitidwe 19:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Tsopano mukuona ndipo mukumva za Paulo ameneyu, kuti si mu Efeso+ mokha muno mmene wakopa anthu ambirimbiri ndi kuwapatutsira ku chikhulupiriro china. Wachita zimenezi pafupifupi m’chigawo chonse cha Asia. Iye akumanena kuti milungu yopangidwa ndi manja+ si milungu ayi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena