26 Tsopano mukuona ndiponso mukumva zoti Paulo wakopa anthu ambiri kuti ayambe kukhulupirira zinthu zina. Wachita zimenezi osati mu Efeso+ mokha muno, koma pafupifupi mʼchigawo chonse cha Asia. Iye akumanena kuti milungu yopangidwa ndi manja si milungu ayi.+