Machitidwe 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho, popeza ndife ana a Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa ndi anthu aluso.+ 1 Akorinto 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano si kanthu+ ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+
29 Choncho, popeza ndife ana a Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa ndi anthu aluso.+
4 Ndiyeno pa nkhani ya kudya zakudya zoperekedwa kwa mafano, timadziwa kuti fano si kanthu+ ndiponso kuti kulibe Mulungu wina koma mmodzi yekha.+