Machitidwe 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:29 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 146 Nsanja ya Olonda,7/15/2010, ptsa. 30-311/15/2004, tsa. 32
29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+