Yesaya 44:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kwa aliyense amene wapanga mulungu kapena kuumba fano lopangidwa ndi chitsulo chosungunula,+ lidzakhala lopanda phindu ngakhale pang’ono.+ Yeremiya 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kodi munthu wochokera kufumbi angapange milungu? Zimene munthu amapangazo si milungu yeniyeni.+ Habakuku 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi chifaniziro chosema, chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndiponso mphunzitsi wonama,+ zili ndi phindu lanji+ kuti wozipanga azizikhulupirira+ ndipo azipanga milungu yopanda pake yosalankhula?+
10 Kwa aliyense amene wapanga mulungu kapena kuumba fano lopangidwa ndi chitsulo chosungunula,+ lidzakhala lopanda phindu ngakhale pang’ono.+
18 Kodi chifaniziro chosema, chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndiponso mphunzitsi wonama,+ zili ndi phindu lanji+ kuti wozipanga azizikhulupirira+ ndipo azipanga milungu yopanda pake yosalankhula?+