Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 115:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mafano awo ndi opangidwa ndi siliva ndi golide,+

      Ntchito ya manja a munthu wochokera kufumbi.+

  • Yesaya 46:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pali anthu amene amakhuthula golide m’zikwama, ndi kuyeza siliva pasikelo. Iwo amalemba ganyu mmisiri wa zitsulo ndipo iye amapanga mulungu ndi zinthu zimenezi.+ Kenako anthuwo amayamba kuweramira ndi kugwadira mulunguyo.+

  • Yeremiya 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Akatero amakongoletsa fanolo ndi siliva komanso golide.+ Kenako amatenga nyundo ndi kukhomerera mafanowo pansi ndi misomali kuti asagwe.+

  • Hoseya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma iye sanavomereze+ kuti ndine amene ndinali kumupatsa mbewu,+ vinyo wotsekemera* ndi mafuta. Sanavomerezenso kuti ndine amene ndinamuchulukitsira siliva ndi golide amene iye anali kumugwiritsa ntchito popembedza Baala.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena