Deuteronomo 32:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti iwo ndi mtundu wopanda nzeru,+Ndipo ndi osazindikira.+ Yesaya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ng’ombe yamphongo imam’dziwa bwino munthu amene anaigula, ndipo bulu amadziwa chinthu chimene mbuye wake amam’dyetseramo. Koma Isiraeli sandidziwa,+ ndipo anthu anga sanachite zinthu mozindikira.”+
3 Ng’ombe yamphongo imam’dziwa bwino munthu amene anaigula, ndipo bulu amadziwa chinthu chimene mbuye wake amam’dyetseramo. Koma Isiraeli sandidziwa,+ ndipo anthu anga sanachite zinthu mozindikira.”+