Deuteronomo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Yehova adzakutumizira matemberero,+ chisokonezo+ ndi chilango+ pa ntchito zako zonse zimene ukuyesa kugwira. Adzakuchitira zimenezi kufikira utafafanizidwa ndi kutha mofulumira, chifukwa cha kuipa kwa zochita zako popeza kuti wandisiya.+ Yeremiya 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mphepo yamphamvu ikuchokera m’njirazo kubwera kwa ine. Ine ndidzawauza ziweruzo zanga.+
20 “Yehova adzakutumizira matemberero,+ chisokonezo+ ndi chilango+ pa ntchito zako zonse zimene ukuyesa kugwira. Adzakuchitira zimenezi kufikira utafafanizidwa ndi kutha mofulumira, chifukwa cha kuipa kwa zochita zako popeza kuti wandisiya.+