1 Samueli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero Afilisiti anamenyadi nkhondo, ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense wa iwo anayamba kuthawira kuhema wake.+ Ndipo amene anaphedwa anali ochuluka kwambiri.+ Panaphedwa amuna oyenda pansi a Isiraeli okwanira 30,000.+ 2 Mafumu 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pankhondoyo, Ayuda anagonja pamaso pa Aisiraeli+ moti aliyense anathawira kuhema wake.
10 Chotero Afilisiti anamenyadi nkhondo, ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense wa iwo anayamba kuthawira kuhema wake.+ Ndipo amene anaphedwa anali ochuluka kwambiri.+ Panaphedwa amuna oyenda pansi a Isiraeli okwanira 30,000.+