Salimo 78:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Iye anapereka anthu ake ku lupanga,+Ndipo anakwiyira cholowa chake.+