1 Samueli 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Afilisitiwo anafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo+ kuti amenyane ndi Aisiraeli. Nkhondoyo sinawayendere bwino Aisiraeli, moti anagonjetsedwa ndi Afilisiti.+ Iwo anakantha amuna achiisiraeli pafupifupi 4,000 nkhondoyo ili mkati. 1 Samueli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero Afilisiti anamenyadi nkhondo, ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense wa iwo anayamba kuthawira kuhema wake.+ Ndipo amene anaphedwa anali ochuluka kwambiri.+ Panaphedwa amuna oyenda pansi a Isiraeli okwanira 30,000.+ Yeremiya 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi+ m’mizinda ya Yuda ndi m’misewu ya Yerusalemu pakuti dzikoli lidzakhala litawonongedwa.’”+
2 Afilisitiwo anafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo+ kuti amenyane ndi Aisiraeli. Nkhondoyo sinawayendere bwino Aisiraeli, moti anagonjetsedwa ndi Afilisiti.+ Iwo anakantha amuna achiisiraeli pafupifupi 4,000 nkhondoyo ili mkati.
10 Chotero Afilisiti anamenyadi nkhondo, ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense wa iwo anayamba kuthawira kuhema wake.+ Ndipo amene anaphedwa anali ochuluka kwambiri.+ Panaphedwa amuna oyenda pansi a Isiraeli okwanira 30,000.+
34 Pamenepo ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi+ m’mizinda ya Yuda ndi m’misewu ya Yerusalemu pakuti dzikoli lidzakhala litawonongedwa.’”+