Yoswa 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Isiraeli sadzathanso kulimbana ndi adani awo.+ Iwo azingothawa kwa adani awo, chifukwa iwonso akhala zinthu zoyenera kuwonongedwa. Sindidzakhalanso nanu kufikira mutachotsa pakati panu zinthu zoyenera kuwonongedwazo.+ Salimo 44:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma tsopano mwatitaya ndi kutichititsa manyazi,+Simukuyenda ndi magulu athu ankhondo.+ Salimo 79:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti iwo awononga mbadwa zonse za Yakobo,+Ndipo malo ake okhalamo awasandutsa bwinja.+ Salimo 106:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+
12 Ana a Isiraeli sadzathanso kulimbana ndi adani awo.+ Iwo azingothawa kwa adani awo, chifukwa iwonso akhala zinthu zoyenera kuwonongedwa. Sindidzakhalanso nanu kufikira mutachotsa pakati panu zinthu zoyenera kuwonongedwazo.+
41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+Kuti anthu odana nawo awalamulire,+