Salimo 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+N’chifukwa chiyani mwanditaya?Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?+ Salimo 74:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 74 Inu Mulungu, n’chifukwa chiyani mwatitaya?+N’chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira nkhosa zimene mukuweta?+
2 Pakuti inu ndinu Mulungu wanga, ndinu malo anga achitetezo.+N’chifukwa chiyani mwanditaya?Ndikuyenderanji wachisoni chifukwa choponderezedwa ndi mdani wanga?+
74 Inu Mulungu, n’chifukwa chiyani mwatitaya?+N’chifukwa chiyani mkwiyo wanu ukuyakira nkhosa zimene mukuweta?+