Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 39:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mwa kudzudzula cholakwa, mwawongolera munthu,+

      Ndipo mwawononga zinthu zake zamtengo wapatali ngati mmene njenjete*+ imachitira.

      Ndithudi, munthu aliyense ali ngati mpweya.+ [Seʹlah.]

  • Salimo 80:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Watenthedwa ndi moto ndi kudulidwa.+

      Iwo amawonongeka ndi kudzudzula kwa pankhope panu.+

  • Yesaya 30:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Anthu 1,000 adzanjenjemera chifukwa cha mawu oopseza a munthu mmodzi.+ Ndipo chifukwa cha mawu oopseza a anthu asanu, inuyo mudzathawa mpaka mudzatsala ochepa ngati mtengo wautali wa pangalawa wozikidwa pamwamba pa phiri, ndiponso ngati mtengo wozikidwa pamwamba pa phiri laling’ono kuti ukhale chizindikiro.+

  • Yesaya 51:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ana ako akomoka.+ Agona m’misewu yonse ngati nkhosa zakutchire zokodwa mu ukonde,+ ngati anthu okhuta mkwiyo wa Yehova,+ okhuta kudzudzula kwa Mulungu wako.”+

  • Ezekieli 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Udzakhala chitonzo+ ndi chinthu chochilankhulira mawu onyoza.+ Udzakhalanso chenjezo+ ndi choopsezera mitundu yokuzungulira ndikadzakuweruza mokwiya komanso mwaukali, ndiponso ndikadzakulanga mokwiya.+ Ineyo Yehova ndi amene ndanena zimenezi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena