Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Mizinda yanu ndidzaiwononga ndi lupanga+ ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu,+ komanso sindidzalandira nsembe zanu zafungo lokhazika mtima pansi.+

  • Deuteronomo 4:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 ndikutenga kumwamba ndi dziko lapansi+ lero monga mboni zokutsutsani, kuti mudzafafanizidwa mwamsanga m’dziko limene mukupita kukalitenga mutawoloka Yorodano. Simudzatalikitsa masiku anu m’dzikomo chifukwa mudzawonongedwa ndithu.+

  • Yoswa 23:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Adzatero chifukwa chakuti mwaphwanya pangano la Yehova Mulungu wanu limene anakulamulani, ndiponso chifukwa chakuti mwapita kukatumikira milungu ina ndi kuigwadira.+ Pamenepo, mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani+ ndipo mudzatha mwamsanga padziko labwino limene iye anakupatsani.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena