Deuteronomo 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndaika moyo ndi imfa, dalitso+ ndi temberero+ pamaso panu.+ Kumwamba ndi dziko lapansi ndi mboni pa zochita zanu.+ Choncho inuyo ndi mbadwa zanu+ musankhe moyo kuti mukhalebe ndi moyo.+ Deuteronomo 31:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Sonkhanitsani akulu onse a mafuko anu ndi atsogoleri anu,+ kuti ndilankhule mawu awa m’makutu mwawo, ndipo nditenge kumwamba ndi dziko lapansi kukhala mboni zanga pamaso pawo.+ Yesaya 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+
19 Ndaika moyo ndi imfa, dalitso+ ndi temberero+ pamaso panu.+ Kumwamba ndi dziko lapansi ndi mboni pa zochita zanu.+ Choncho inuyo ndi mbadwa zanu+ musankhe moyo kuti mukhalebe ndi moyo.+
28 Sonkhanitsani akulu onse a mafuko anu ndi atsogoleri anu,+ kuti ndilankhule mawu awa m’makutu mwawo, ndipo nditenge kumwamba ndi dziko lapansi kukhala mboni zanga pamaso pawo.+
2 Imvani+ kumwamba inu, ndipo tchera khutu iwe dziko lapansi, chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndalera ana ndi kuwakulitsa,+ koma iwo andipandukira.+