Deuteronomo 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Onani, ndikukuikirani pamaso panu lero dalitso ndi temberero:+ Deuteronomo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Madalitso onsewa adzakutsata ndi kukupeza+ chifukwa ukumvera mawu a Yehova Mulungu wako: