Deuteronomo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mudzalandira madalitso onsewa ndipo zinthu zabwino zonsezi zidzakhala zanu,+ mukapitiriza kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu: Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:2 Nsanja ya Olonda,12/15/2010, ptsa. 19-209/15/2010, tsa. 89/15/2001, tsa. 10
2 Mudzalandira madalitso onsewa ndipo zinthu zabwino zonsezi zidzakhala zanu,+ mukapitiriza kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu: