15 Ngati kutumikira Yehova kukukuipirani, sankhani lero amene mukufuna kum’tumikira,+ kaya milungu imene makolo anu amene anali kutsidya lina la Mtsinje anatumikira,+ kapena milungu ya Aamori amene mukukhala m’dziko lawo.+ Koma ine ndi a m’nyumba yanga, tizitumikira Yehova.”+