Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 24:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mukasiya Yehova+ n’kuyamba kutumikira milungu yachilendo,+ iyenso adzakutembenukirani ndithu, n’kukuchitirani zoipa ndi kukufafanizani, pambuyo pokuchitirani zabwino.”+

  • 2 Mafumu 22:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 chifukwa chakuti andisiya n’kumakafukiza nsembe yautsi kwa milungu ina+ kuti andikwiyitse ndi ntchito zonse za manja awo.+ Choncho mkwiyo wanga wayakira malo ano ndipo suzimitsidwa.’”’+

  • 2 Mbiri 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma inuyo mukadzabwerera+ n’kusiya kutsatira malamulo anga+ amene ndakupatsani, komanso mukadzapita kukatumikira milungu ina+ ndi kuigwadira,+

  • Yeremiya 17:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Inu Yehova, chiyembekezo cha Isiraeli,+ onse amene akukusiyani adzachita manyazi.+ Mayina a anthu onse okupandukirani+ adzalembedwa pafumbi chifukwa asiya Yehova magwero a madzi amoyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena