Salimo 115:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mafano awo ndi opangidwa ndi siliva ndi golide,+Ntchito ya manja a munthu wochokera kufumbi.+ Yesaya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo. Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.+ Yesaya 44:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma mtengo wotsalawo wapangira mulungu, wapangira chifaniziro chake chosema. Wachiweramira ndi kuchigwadira n’kumapemphera pamaso pake kuti: “Ndipulumutseni, pakuti ndinu mulungu wanga.”+ Mika 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzagwetsa zifaniziro zanu zogoba ndi zipilala zopatulika zimene zili pakati panu, ndipo simudzagwadiranso ntchito za manja anu.+
8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo. Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.+
17 Koma mtengo wotsalawo wapangira mulungu, wapangira chifaniziro chake chosema. Wachiweramira ndi kuchigwadira n’kumapemphera pamaso pake kuti: “Ndipulumutseni, pakuti ndinu mulungu wanga.”+
13 Ndidzagwetsa zifaniziro zanu zogoba ndi zipilala zopatulika zimene zili pakati panu, ndipo simudzagwadiranso ntchito za manja anu.+