Yesaya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo. Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.+ Yesaya 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye sadzayang’ana maguwa a nsembe,+ omwe ndi ntchito ya manja ake.+ Sadzayang’anitsitsa zimene zala zake zapanga, kaya mizati yopatulika kapena maguwa ofukizirapo zonunkhira.+ Ezekieli 36:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ine ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera. Ndidzakuyeretsani+ pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+ Hoseya 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+ Sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!” chifukwa inu mumachitira chifundo mwana wamasiye.’*+ Zekariya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wa makamu wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzathetsa mayina a mafano m’dziko lonseli+ ndipo mafanowo sadzakumbukiridwanso. M’dzikoli ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.+
8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo. Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.+
8 Iye sadzayang’ana maguwa a nsembe,+ omwe ndi ntchito ya manja ake.+ Sadzayang’anitsitsa zimene zala zake zapanga, kaya mizati yopatulika kapena maguwa ofukizirapo zonunkhira.+
25 Ine ndidzakuwazani madzi oyera ndipo mudzakhala oyera. Ndidzakuyeretsani+ pokuchotserani zonyansa zanu zonse+ ndi mafano anu onse onyansa.+
3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+ Sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!” chifukwa inu mumachitira chifundo mwana wamasiye.’*+
2 Yehova wa makamu wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzathetsa mayina a mafano m’dziko lonseli+ ndipo mafanowo sadzakumbukiridwanso. M’dzikoli ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.+