Yesaya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo. Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.+ Hoseya 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zimenezi zachokera ku Isiraeli.+ Mmisiri ndiye anapanga fano la mwana wa ng’ombe la ku Samariya.+ Fanolo si Mulungu woona, chifukwa lidzangokhala ngati nkhuni zowazawaza.+ Mika 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzagwetsa zifaniziro zanu zogoba ndi zipilala zopatulika zimene zili pakati panu, ndipo simudzagwadiranso ntchito za manja anu.+
8 Dziko lawo ladzaza ndi milungu yopanda phindu.+ Iwo amagwadira ntchito ya manja awo. Amagwadira chinthu chimene zala zawo zapanga.+
6 Zimenezi zachokera ku Isiraeli.+ Mmisiri ndiye anapanga fano la mwana wa ng’ombe la ku Samariya.+ Fanolo si Mulungu woona, chifukwa lidzangokhala ngati nkhuni zowazawaza.+
13 Ndidzagwetsa zifaniziro zanu zogoba ndi zipilala zopatulika zimene zili pakati panu, ndipo simudzagwadiranso ntchito za manja anu.+