4 Yehova, pogwiritsa ntchito mzimu wa chiweruzo ndi mzimu wa moto,+ adzatsuka nyansi za ana aakazi a Ziyoni,+ ndiponso adzatsuka+ mkati mwa Yerusalemu n’kuchotsamo magazi amene Yerusalemuyo anakhetsa.+
11 Ndipo ena mwa inu munali otero.+ Koma mwasambitsidwa kukhala oyera,+ mwapatulidwa,+ mwayesedwa olungama+ m’dzina la Ambuye wathu Yesu Khristu,+ komanso ndi mzimu wa Mulungu wathu.+